Home » GULU LA ANYAMATA OYIMBA ALI PA CHITHUNZIWA, FUGITIVO, LAPHEDWA.

GULU LA ANYAMATA OYIMBA ALI PA CHITHUNZIWA, FUGITIVO, LAPHEDWA.

Ku Mexico, gulu la anyamata oyimba ali pa chithunziwa, Fugitivo, laphedwa.
Anapangidwa book kuti akayimbe kwina kwake. Yemwe ali kumanzeleyo anafika pomwe amayenera kukumana mochedwa nkupeza ena onsewo palibepo.
Iyeyo amawona ngati amuthawa, nde anabwelera.
Zitadziwika kuti anthu aja (3, plus manager wawo), asowa, a Polisi anayamba kuwasaka.
Apezeka mgalimoto pafupi ndi border ya US ataphedwa. Ena akuti atawotchedwa.
Mphekezera zikuti aphedwa ndi magulu ogulitsa ma drug, omwe avuta ku Mexico – wa.
Zinafika poti oyimba amawopsyezedwa kuti azipereka msonkho kwa maguluwa, komanso aziyimba nyimbo zowatamanda. Kupanda kutelo, anthu amaphedwa.

The Grupo Fugitivo, a regional Mexican band full of rhythm and rising dreams, was booked to perform in late May 2025. It was supposed to be another night of music. But only silence followed. One member arrived late to the meeting point — the others had vanished. He thought they’d moved on without him. But it was far worse.

Why would musicians be murdered? In northern Mexico, the music scene — especially those who play narcocorridos, songs that depict drug lords and criminal exploits — has long been entangled with organized crime. Cartels often coerce or commission musicians to sing their praises. Refusing to comply can mean death. Compliance, too, is no guarantee of survival.

The authorities arrested suspects connected to the cartel, including a known leader. Yet, even now, questions burn hotter than answers. Families of the victims remain unconvinced, pointing to a lack of clear evidence, no identification, no belongings — just silence and ash.

Meanwhile, candles flicker across Reynosa. Protesters march. Guitars remain still. The rhythm of life continues, but the echo of what happened to Grupo Fugitivo plays on — a mournful ballad in a land where music, culture, and danger are tragically entwined.

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *